Za Daniel Phiri Ndikumva Ndiiwe Mwina Unampatsa Ndiiwe Poti Ndiwe Pilirani Phiri…

Pilirani Phiri; “potsatira kutuluka kwa lipoti la imfa ya Bingu pali chyembekezo kuti inu a Kaliati muntha kumangidwa, muli ndi mantha??

Patricia Kaliati;
“Ha, ha, ha, pilirani ine Patricia Kaliati mwana wa botomani ndilibe mantha.”

Pilirani Phiri; “komatu lipoti likusonyeza kuti mumafuna kulanda boma?”

Patricia Kaliati; ” Timafuna kulanda boma lake liti, popeza nthawi imeneyo panalibe amene analumbiritsidw ­a kuti akhale mtsogoleri koma inu muziopa mulungu.”

Pilirani Phiri; “Lipoti likunenanso kuti mamafuna kuti Peter wa mutharika kuti atenge mpando wautsogoleri wa dziko lino”

Patricia Kaliati; “ndichifukwa chake mulungu akukulangani, chimanga thumba limodzi K10,000 Simunati Mulungu azikulanganibe. ­”

Pilirani Phiri;
“zinakhala bwanji kuti Bingu akhale Daniel Phiri pamene amapita naye kuchipatala ku South Africa, munabalalika kwambiri eti?”

Patricia Kaliati;
“za Daniel Phiri ndikumva ndiiwe mwina unampatsa ndiiwe poti ndiwe pilirani Phiri.

You May Also Like

21 NDEMANGA

  1. Ukuyakha boo! Patricia …..kumwalira president zinthu sizimakhala bwino asamakuvuteni munayesesa chifukwa pakanakhala nkhondo koma Tinasunga bwino maliro….

  2. Ati amafuna kulanda boma ? boma lakedi liti ngati analipo amene anamulumbiritsa boma lake lungopanga za phadali.Komanso apilirani mumuuze anutulutsa report yo akayambenso kachikenanso mwina analakwitsa kapena ankafuna kunena UDF kapenanso ankafunanso unduna kaya anali wakunja ankafuna citizenship mutifunsileko kwa abwanawo

  3. Bima lake liti?.monga iyeyu sakuwabe malamulo pa nkhani ya president ndi vice-president.ngati kunalibe boma kapena mtsogoleri ndi chifukwa chani sitidavotenso

  4. I think and hope Malawi is going to an end guys.Let’s put everything in the hands of our Almighty father to guide Malawi as a nation.To be very kind and clear,Malawi is facing alot of economic crisis and no matter what it takes,will never ever be a proud Malawi. Each and everyone think only about his or her family.Lack of honest leadership in our country. We shall remain behind till I don’t know.

  5. Ndemanga:this is crazy,the muntharikaz awononga boma iri guys mpaka 50 KGS 12 thousand kwacha shaaa

ZIMENE MUMAKONDA

Please enter your comment!
Please enter your name here

From The World