Men who beheaded a Ndirande girl now in jail

Anthu oposa 10 ali mmanja mwa
apolice ku BT kaamba kopha ndi
kudula mutu mtsikana ku Ndirande. Dzulo apolice adangwira mzake wa
malemuyu kukamufunsa mafunso
ndipo iye sadabise kuti adatengedwa
ndi ana a MR PASELI omwe adabwela
ndi magalimoto onyezimila.
Kenaka apolice lelo agwira anyamata atatu omwe ndi Ana mr. Paseli

Mtsikanayo adali ndi zaka 18 ndipo
mutu ndi mtima sizikudziwika komwe
zidapita

 

Story here http://www.faceofmalawi.com/2013/05/ndirande-propstitute-found-headless/

5 thoughts on “Men who beheaded a Ndirande girl now in jail

  1. Zosakhala boh ..kwen kwen mkulu amenei Bwanj….. alandile chilango mosakondela…poti dziko lakwathukoso limakomela achuma okha

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *