A police ku Balaka amanga mayi wina wa zaka 23, Beatrice Kalimanjolo, kamba kotenga msomali wa 4 inches ndikuwukhoma pa dzanja la mwana wake mpakana nsomali wo kutulukira mbali inayi ya dzanja.

Mayi Beat ati anapanga izi chifukwa mwanayo anaba K200 imene amafuna kukagulako ndiwo ndikuyiwononga

You May Also Like

2 NDEMANGA

ZIMENE MUMAKONDA

Please enter your comment!
Please enter your name here

From The World