kodi zomwe wachita Josephy Kamwendo yemwenso ndi captain wa malawi national team popanga post chithuzi chomwe chikuonesa anyamata a Nigeria akukondwelera chigoli chawo m’mene amasewela ndi flames ndizolondola? kutengela kuti iye ndi captain.
kodi akanakamenya game imeneyi akanapanga zimenezi?
nanga kodi anasiidwa ndi yekha?
three words for JK .
Former Flames Captain, Joseph Kamwendo, who was dropped from the squad to face Nigeria due to undisclosed reasons by Coach Saintfeit has posted a picture on his facebook page of Nigeria Players celebrating one of their goals against the Flames.
Kamwendo wapangira izi chikuwawe akuti.
Ameneyu ndi psiru ndithu. Asazabwerenso kuno azikakhala ku Nigeria