HOME Politics Elections 2019 Ma Black Akana Kulandira “Banzi” Lo Chokera Ku Dpp

Ma Black Akana Kulandira “Banzi” Lo Chokera Ku Dpp

0
2129

Mphekesera ikumveka kuti Ma blacks (Black Missionaries) akuti dzulo akana kulandira ndalama zoti akamenye show ya ulere la mulungu Ku Blantyre pofuna kuti anthu ambiri asazapite Ku sonkhano wa UTM

Ma report akusonyeza  kuti Ma blacks ayankha kuti Ali ndi show ina ndipo sangawawuze zochita mu masiku ochepa kuti akaimbe pa mwambo wo tsegulira Kamuzu stadium.

Zikumveka kuti m’modzi mwa oyimba amene amafuna akathandizane ndi ma blacks anasankhidwa ndi katswiri Taygrin.

More to come…..

PALIBE NDEMANGA

ZIMENE MUMAKONDA

Please enter your comment!
Please enter your name here