Nkulu wina yemwe dzina lake silikudziwika wokonda khalidwe lopanga chisembwele ndi azimayi oyenda yenda[Mahule],waona mbwadza atakoma atamwa makhwala owonjezela mphamve kubedi pokonzekela mzimayi wina yemwe anagwilizana naye.

Malingana ndi tsamba la nchezo lapa intaneti lotchedwa facebook,Nkuluyi akuti anagwiliza ndi m’mayi wina kuti akumane malo ena ogona alendo ntaunimu.Ndipo podikila nkuluyu anamwa makhwala owonjezela mpamvu kubedi otchedwa nkwapukwapu.

Tsoka ilo mbendu anagwizananayo ija inapezeka kuti sinabwele ku malo ogona alendo anagwilizanawo,kotelo kuti nkuluyi zinamuvuta mpaka anakomoka nawo makhwalawo poti sanagwile ncthito yake bwinobwino.

M’musimu ndi zina mwa zithuzi zomwe zili pa tsamba la nchezo la intaneti  lotchedwa facebook  za nkuluyi ndi ena omwe anamupeza nkuliyu

.

You May Also Like

ZIMENE MUMAKONDA

Please enter your comment!
Please enter your name here

From The World