Za Daniel Phiri Ndikumva Ndiiwe Mwina Unampatsa Ndiiwe Poti Ndiwe Pilirani Phiri…

Pilirani Phiri; “potsatira kutuluka kwa lipoti la imfa ya Bingu pali chyembekezo kuti inu a Kaliati muntha kumangidwa, muli ndi mantha??

Patricia Kaliati;
“Ha, ha, ha, pilirani ine Patricia Kaliati mwana wa botomani ndilibe mantha.”

Pilirani Phiri; “komatu lipoti likusonyeza kuti mumafuna kulanda boma?”

Patricia Kaliati; ” Timafuna kulanda boma lake liti, popeza nthawi imeneyo panalibe amene analumbiritsidw ­a kuti akhale mtsogoleri koma inu muziopa mulungu.”

Pilirani Phiri; “Lipoti likunenanso kuti mamafuna kuti Peter wa mutharika kuti atenge mpando wautsogoleri wa dziko lino”

Patricia Kaliati; “ndichifukwa chake mulungu akukulangani, chimanga thumba limodzi K10,000 Simunati Mulungu azikulanganibe. ­”

Pilirani Phiri;
“zinakhala bwanji kuti Bingu akhale Daniel Phiri pamene amapita naye kuchipatala ku South Africa, munabalalika kwambiri eti?”

Patricia Kaliati;
“za Daniel Phiri ndikumva ndiiwe mwina unampatsa ndiiwe poti ndiwe pilirani Phiri.

(Visited 93 times, 1 visits today)

0

Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram