Uku nde Kuidelera Flames:Timu ya mpira ya dziko la Zimbabwe yomwe imadziwikanso kuti the Warriors sinaseweleko training ina iliyonse pokonzekera Malawi,moti ma player angochoka mmanyumba mwakwawo nkumabwera kuno,mphuzitsi wa timuyi wati izi siziwakhuza kwenikweni chifukwa choti ma player awo ambili anali active mu league yamdzikomo..ma flames otchani anthuwa,ife zotizolowera timadana nazo.

(Visited 6 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram