MUNTHU WINA WA KU NTAJA M’BOMA LA MACHINGA YEMWE ADAMWALIRA M’CHAKA CHA 2007 WAPEZEKA ALI MOYO MU TEA ROOM INA PA LIWONDE AKUMWA TEA, KOMA AKULEPHERA KULANKHULA MOTI
AKUGWIRITSA SIGN LANGUAGE, MWAMWAI WAKUMANA NDI M’BALE WAKE AMENE WAMUTENGA KUBWERERA NAE KU NTAJA PA CAR HIRE POPEZA ANTHU ANATHAWA MINBUS YOMWE ANAKWERA
ATAZINDIKILA KUTI AKWERA NDI MZUKWA.

(Visited 11 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram