Malawi’s dance hall artiste Wendy Harawa was arrested on Wednesday by Chileka Police for duping Mwanza Motel K240,000 in advance payment for a show which never was.

We are sure it was just logistical hiccups Wendy ndi mzimayi waulemu wake sikuti anali ncholinga chakuba ayi!

A police ku Chileka dzulo anatsekera mu chitokosi oyimba otchuka wa mkazi, Wendy Harawa, kamba koponda ndalama zokwana K280, 000.
Ndalamazi anapatsidwa ndi a Mwanza Motel ngati advance payment kuti Wendy yu azapite akapangitse show ku Motel ko koma atangolandira msungwana oyimba yi sanapitekonso ndipo atawuzidwa kuti abwenze amangoyankha miyala.

Eni Mwanza Motel pokwiya anangomumangitsa ndipo ndalama zimene anapondazi abwenza ndi achibale ake

(Visited 11 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram