Patangodutsa masiku ochepa mbava zitathyola office za Malawi Post Cooperations (MPC) ndikuba katundu wandalama zambiri, mbavazi zinabweleranso usiku wapitawu ndikukakatulanso ma office ena eight ndikuba katundu wambiri monga ma computer, camera ndi zina zambiri.

Chokhumudwitsa ndichakuti, mbavazi zisana kakatule ma office wa, zinayamba zakupa makofi ndi kumanga alonda a company ina ya ku UK omwe ndi amene amalondera malowa.

(Visited 24 times, 1 visits today)

0

Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram