Mtsogolero wa chipani cha DPP Professor Author Peter Muthalika tsopano azidziwika ndi dzina loti’ Joshua wa lero’.

Dzinali, linadza kudzera pamkumano womwe achinyamata anachititsa pa Chigumula Admarc Ground mumzinda wa Blantyre womwe cholinga chake chinali kupempha mphamvu ya ambuye kuti itsogolere Peter panthawi ino yomwe akukumana ndiziphinjo zosiyanasiyana.

Malingana ndi mkulu owona nkhani zachipembezo muchipani cha DPP bambo Wells Adamz, Peter Muthalika wavala dzinali kuyambila lero.

(Visited 11 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram