Apolisi ku Blantyre, akusunga m’chitolokosi munthu yemwe akumuganizila kuti, anaba ndalama zokwana K20,000 ndi ma degree awiri kunyumba ya Nduna yowona za malo ndi zomangamanga bambo Henry Phoya kunyumba yawo yawo ku Chigumula.

Malingana ndi report lomwe latipeza, munthuyu ati anali wantchito wa ku nyumba ya bambo Phoya koma anangothawa ndi ndalama komanso ndi degree ya olemekeza wa pamodzi ndi ya akazi awo.

(Visited 9 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram