Concerned consumers are set to hold anti-government protests tomorrow in Blantyre over what they call President Joyce Banda’s failure to respond to a petition by the Consumers Association of ‪#‎Malawi‬ (CAMA).

Failure by President Banda to declare her assets and her frequent travels are some of the issues they are planning to protest against.

Bambo Chawanangwa Msukwa akudziwitsa anthu aku Blantyre ndi madera ozungulira kuti ma demo okwiya ndi kukwela mitengo kwa katundu alipo m’mawa pa 17 July.

A Msukwa akuti anthu akasonkhana kaye pa Kamuzu Upper Stadium kenaka ndikukaguba ulendo wopita kukapeleka petition kwa a CEO a BT City Council, Bwana Ted Nandolo.

A Msukwa ati ma demo akhalapo ngakhale a Police akufuna azichuluka nzeru kuti alepheleke.

(Visited 33 times, 1 visits today)


Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram