In the lot for Mzuzu deliveries his offer price was mk112/kg but contract offered to someone supplying at mk120/kg

In the lot for Luchenza deliveries, Mulli offered to deliver at mk110/kg but other bidders at mk125 won…

Where is value for money?

Meaniwhile

Namandwa wa business m’dziko muno komanso mkulu wa Mulli Group of Companies Leston Mulli wati wafinyidwa kolapitsa ndi boma la mayi Joyce Banda.

Malingana ndi Mulli, zomwe zamupangitsa jenkhaaa ndizomwe lachita boma posachedwapa posamugula chimanga, ngakhale kuti iye ananena motsimikiza kuti chimanga ali nacho choti atha kudyetsa dziko lonse lino ingakhale zaka ziwiri.

Koma Mulli wati ndiwodabwa kuti boma lasankha kugula chimangachi kunja kwa dziko lino pomwe iye chake chili poteropo zomwe zikuwonetseratu kuti boma la mayi Joyce Banda likuchita naye nsanje.

(Visited 18 times, 1 visits today)


Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram