Malawi will need to raise K500 million in order to repatriate Rwandan refugees as part of United Nations High Commission for Refugees (UNHCR)’s Cessation Clause that came into effect on June 30 this year, Home Affairs Minister Uladi Mussa has said.
Ma Burundi anabwera ku Malawi kuno ngati ma refugee kufuna chitetezo kamba koti kwawo kunali nkhondo. Sanabwere kuno kudzapanga business yi ndiye sizolondola kuti azitero. tiwatolere amenewa azipita kwawo kapena akasiyidwe kudzaleka

– Mfumu ya ku Dedza yakamba zimenezi. Mukugwirizana nazo kapena ayi?

(Visited 21 times, 1 visits today)


Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram