A 14 year old girl has been admitted at the Mangochi District Hospital after being gang-raped by 6 men.

Msungwana yu yemwe achita kumupopa zi ukala zochuluka anathilidwa, amusokanso ku maliseche kwake kumene kunang’ambika komanso wapatsidwa mankhwala omwe amwe kwa 30 days kuti ngati m’modzi omugwililirawo anali HIV positive, asayitenge nawo

A police ku Mangochi anena kuti akufufuza midala inapanga zachipongwezi

(Visited 9 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram