Sally Nyundo watisiya dzulo mdziko
muno pamene wanyamuka ulendo
wake okaimba mu dziko la Canada. Tikakamba za maimbidwe abwino ku
Malawi kuno Sally Nyundo ekha
sangalephere.

Sally Nyundo ndi uja anaimba nyimbo
monga Ras amadya mzimbe,kukuched
wa kucha,Jah bless me komanso
anaimbapo nyimbo ndi malemu
Mafunyeta(mzimu wake uuse mu
mtendere) nyimbo yoti this girl is hot.

Tingomufunira zabwino zonse man
Sally. Mverani Nyimbo za Sally apa http://www.malawi-music.com/

(Visited 6 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram