suitcaseMdyomba uyu waku Mangochi wagwidwa pa BEIT BRIDGE pomwe anabisala mu Expand ndicholinga choti avenche mu South Africa kamba koti analibe passport.

Mdyombayu wapezekanso ndi kachithumwa komwe ati ntchito yake ndiyoti amawafoilitsa azungu mitu ku joweniko ku azimupatsa ndalama zambiri komanso katundu.

(Visited 4 times, 1 visits today)
0
Subscribe to our Youtube Channel :