
Mwana apanidwa ndi Mtengo
Published on March 8, 2018 at 4:24 PM by Robert Ngwira
Chipwilikiti chinabuka m’mudzi wina mwana yemwe amasewera pa mpata omwe uli pa mtengo wina kumeneko atakanilira.
Malipo omwe sambali lapedza ndiloti mtengowo ndi wamizimu.
Kodi mukuganiza kuti anthu a mmudzi wu apange bwanji kuti amuchotse mwana powonesesanso kuti asamupweteke?