Anthu okhala mu m’zinda wa Lilongwe ayembekezere kuvuta kwamadzi miyezi ikubwerayi.

Lilongwe Watete Board (LWB) anena kuti madzi ndiochepa ku Damu losungila ku Kamuzu Dam. izi zikhala chomwechi kamba kakuchepa kwa mvula m’chakachi.

Wamkulu oyang’anila Lilongwe Water Board Alfonso Chikuni wanena kuti Damuli lidango dzadza ndika mlingo kochepa kokha kotero madera ambiri ku Lilongwe samalandira madzi mokwanira.

(Visited 1 times, 1 visits today)
0

Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram