Bwalo Lamilandu Lalikulu Lipeleka Chilango Kwa Misozi Chanthunya Lero

Bwalo Lamilandu Lalikulu Lipeleka Chilango Kwa Misozi Chanthunya Lero

Published on September 2, 2020 at 5:56 AM by Face of Malawi

55 words • approx. 1 min read

Bwalo lamilandu lalikulu ku Zomba lero likuyembekezeka kupereka chilango kwa Misozi Chanthunya atapezeka olakwa sabata yatha pamlandu opha bwezi lake Linda Gasa mu Chaka Cha 2010.

Oweruza milandu wu Ruth Chinangwa adapezetso a Chanthunya olakwa pamlandu obisa mtembo komanso kunamiza bwalo lamilandu.

Boma lidapempha bwaloli kuti ligamulo a Chanthunya kukhara kundende moyo wawo onse.

Mlembi: Shecks

Subscribe to our Youtube Channel: