Bwalo lamilandu lalikulu ku Zomba lero likuyembekezeka kupereka chilango kwa Misozi Chanthunya atapezeka olakwa sabata yatha pamlandu opha bwezi lake Linda Gasa mu Chaka Cha 2010.

Oweruza milandu wu Ruth Chinangwa adapezetso a Chanthunya olakwa pamlandu obisa mtembo komanso kunamiza bwalo lamilandu.

Boma lidapempha bwaloli kuti ligamulo a Chanthunya kukhara kundende moyo wawo onse.

Mlembi: Shecks

(Visited 59 times, 1 visits today)

0

Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram