Monday, April 29, 2024

Featured Video

Latest Stories

Top 10 Music

Upcoming Events

Fact Up Night

Sat, 04 May 2024 20:00:00 UTC @ Club Casaulina - On 4th May 2024 Achina Gattah Ase and Gibo Pearson will be performing live for Fact Up Night at Club Casaulina in Lilongwe Area 25. The event will start from 8 PM till late More Info
Kapadocia Live In Mzuzu

Sun, 05 May 2024 13:00:00 UTC @ Rose Chanaichi's Gardens - Kapadocia will be performing live in Mzuzu Area 4 at Rose Chanaichi's Gardens on 05 May 2024. He will be supported by Rose Chanaichi Kayira, Motte Jez, Esther Mashani, Chipha Dada, Dele... More Info

Apolisi aku Mozambique anjata asodzi aku Malawi

Apolisi aku Mozambique anjata asodzi aku Malawi kamba kowedza msomba m’nyanja ya Malawi ku gawo la Mozambique.

Asodzi pafupifupi makumi asanu ndi limodzi akumalawi ananjatidwa sabata latha  ndipo malipoti akuonetsa kuti asodziwa  anamasulidwa patapita masiku angapo potengere adindo aku  Malawi atafufuza zankhaniyi.

Koma maboti pafupifupi asanu ndi awiri sanabwezedwe ndi a polisi aku Mozambique.

Apolisi aku Mozambique anena kuti abweza ma botiwo pokhapokha asodiziwo apeleke k5 million kamba powedza  Nsomba popanda chilorezo ku gawo la Mozambique Mu nyanja ya Malawi.

Nyanja a Malawi ili mozunguliridwa ndi maiko a Mozambique ndi Tanzania ndipo nyanjayi maikowa anatengapo gawo pang’ono. Gawo laliku la nyanjali  lidatengedwa ndi dziko la Malawi.

Subscribe to our Youtube Channel:

Related Posts

Face of Malawi
Face of Malawihttps://www.faceofmalawi.com
For more Info: info@faceofmalawi.com

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

Popular Articles