Wednesday, May 1, 2024

Featured Video

Latest Stories

Top 10 Music

[showmfm]

Upcoming Events

[showevents]

“NDITHANDIZENI AKHILISITU”- JOE GWALADI.

M’nyamata woyimba nyimbo mwanthetemya ‘Joe Gwaladi’, wati akupempha ‘akhilisitu’ akufuna kwabwino kuti amuthandize ndi thandizo landalama zoti atulutsire chimbale chake choyamba cha nyimbo za uzimu chomwe akuchitcha ‘Nditamanda Inu’

Malingana ndi Gwaladi, zokonzekera zonse za chimbalechi zatha ndipo chomwe changotsala ndi ndalama zoti ajambulire nyimbo zoonetsa ndi zomvera zomwe zapachimbalechi, koma wati pakadali pano ndalamazo alibe.

Related Posts

6 COMMENTS

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

Popular Articles