Sunday, May 5, 2024

Featured Video

Latest Stories

Top 10 Music

[showmfm]

Upcoming Events

[showevents]

Peter Muthalika holds a dual citizenship

It has now been confirmed that, the Blue Camp leader (a Law Expert himself) Prof. Author Peter Muthalika, will not be allowed to join the political race in 2014 as reports indicate that the he holds a dual citizenship.

Izi zatsimikizika pamene akuluakulu ena aboma, anapita komwe ku America kumene mkuluyu ankakhala ndipo kafukufuku wawo kumeneko wapeza kuti bambo Pitala alidi ndi ‘Dual Citizenship’ kapena kuti ndi mzika ya mayiko awiri (Malawi ndi America) zomwe malingana ndi malamuro adziko lino, ndizosavomerezeka.

According to section 6 and 24 of the Malawi Citizenship Act, any person who at any time while a citizen of Malawi and of full age and capacity, voluntarily claimed and exercised in any other country any right available to him under the law of that country, being a right accorded exclusively to its own citizens, and that it is not conducive to the public good tha he should continue to be a citizen of Malawi shall be liable to deprivation of citizenship of Malawi.

M’mene zateromu, Prof. Author Peter Muthalika ndiye kuti sin’zika yadziko lino ndipo akuyenera kupilikitsidwa kuti azipita kwawo ku America ija mchingerezi timati ‘deport’

Apa ku DPP ndiye kuti yalakwa ndipo ndizachidziwikire kuti anthu awa ndi amene mwina angayimire chipanichi 2014 pampando wawu president.

1) Patricia Akweni Kaliati.

2) Dr. George Chaponda.

3) Lifred Nawena

kapena (4) mayi Jean Kalirani.

Amene wakwera ya DPP aliyense, zimvere Mtolo Prof. Peter Muthalika ‘sayimila 2014 take it or leave it!!!’ Pepani pepani ndithu.

Related Posts

3 COMMENTS

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here

Popular Articles