Facebook

PP’s Msonda shoots at Maulidi

Deputy spokesperson of the ruling Peoples' Party, Ken Msonda, has taken to social media to shoot back at the acting general secretary of the party, Paul Maulidi, who earlier on reported that the party had summoned and suspended him (Msonda) for insubordination. Last week it was indicated that the party had met and had agreed to suspend Msonda after the deputy publicity secretary had gone...

Activist calls for JB return

Controversial human rights activist, Seodi White, has called on President Joyce Banda to return from the US where she is to attend the UN General Assembly. White, who has never been in good books with the JB regime, wrote on her Facebook page that with the current state of affairs in the nation, the state President should come back from her engagement and address the...

Malawian hides in a suitcase to enter SA

Mdyomba uyu waku Mangochi wagwidwa pa BEIT BRIDGE pomwe anabisala mu Expand ndicholinga choti avenche mu South Africa kamba koti analibe passport. Mdyombayu wapezekanso ndi kachithumwa komwe ati ntchito yake ndiyoti amawafoilitsa azungu mitu ku joweniko ku azimupatsa ndalama zambiri komanso katundu.

A DPP A WOTCHA SUKULU YA JOYCE BANDA

Akuluakulu a chipani cholamula boma cha PP ati, sakupenekera konse kuti moto womwe watentha ma hostel anyamata pa sukulu ya Joyce Banda Foundation yaku Chimwankhunda ku Blantyre, anayatsa ndi a chipani cha DPP. ''ife sitikupenekera konse kapena kuchotsera kuti anachita zawupanduzi ndi achipani cha DPP chifukwa sakugona tulo ndi Mayi Joyce Banda. Akufunafuna njira zoti awagonjetse koma akulephera ndinkuwona achita izi. Koma ndiiiiiithu, anjatidwa...

Area 18 porn actor tries to overdose on Penicillin

AMWA OVERDOSE YA Penicillin Myamata wathu Jack Chikapa wa mu A18 ku Lilongwe yemwe anatulutsa ka film kake ka porn ndi bwenzi lake Chisomo, dzulo anamwa penicilin tablets okwana 16 kuti angofa mwayi anapita naye mwachangu ku chipatala kumene anakamuthandiza

Popular

spot_imgspot_img
(Visited 13 times, 1 visits today)