M’nyamata woyimba nyimbo mwanthetemya ‘Joe Gwaladi’, wati akupempha ‘akhilisitu’ akufuna kwabwino kuti amuthandize ndi thandizo landalama zoti atulutsire chimbale chake choyamba cha nyimbo za uzimu chomwe akuchitcha ‘Nditamanda Inu’

Malingana ndi Gwaladi, zokonzekera zonse za chimbalechi zatha ndipo chomwe changotsala ndi ndalama zoti ajambulire nyimbo zoonetsa ndi zomvera zomwe zapachimbalechi, koma wati pakadali pano ndalamazo alibe.

You May Also Like

6 NDEMANGA

  1. Zamlungu kumapangila buzines mmene umatukwanila iwe umati muvu ndi thako kopanda thako no muvu osalowa za chauta ungatukwane namalenge ndi mwana wake.

ZIMENE MUMAKONDA

Please enter your comment!
Please enter your name here

From The World