Bungwe la Malawi Schools Sports Association (MASSA) ladandaula ndizimene anapanga a FAM pomuyitana Gabadinho Mhango ku camp ya Flames komanso pomulowetsa game ya Zimbabwe.

”The game was a friendly one. Gaba is a Form 2 kid. He is suppossed to be in school studying and not playing football. Why FAM called him into camp is just inconsiderate to his future. A FAM akupangilanji zimenezi. Kodi akufuna kuti akanike kulemba mayeso ngati chaka chathanso?” adandaula a MASSA

”kodi nawo a MASSA angothi mfwii mfwiii panopa pamene Gaba yo adasewera kale masewero wo bwanji? Samanena atamutenga ku camp ko bwanji?” a John Kaputa a FAM adabwa motero

(Visited 9 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram