Nsomba zikungofa zokha mu Lake Malawi ndipo ma report osasimikizika akuti A Kayelekera Uranium Mine akumatayamo zotsalira za uranium.

Uranium ndi element yowopsa kwambiri. A Malawi ambiri amadalira madzi amu Lake Malawi wa kumamwa daily ndithu

Zayamba ndi nsomba kenaka timva kuti anthu akungofa ndithu.

Ena akuti boma la Tanzania laponyeramo mankhwala dala chifukwa tikunyaditsa mnyanja yathu

(Visited 6 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram