Munthu mmodzi oyimba
gospel kumalawi kune
otchuka kwambiri ndi dzina
lakuti alan chirwa, dzulo
madzulo analedzela kwambiri
mwakuti zinthu sizinali bwino, amachita
kuseweletsedwa ndi ana
omwe.

Sikuti talemba izi ndicholinga
chomuyalutsa ayi koma
tikufuna achinyamata amene
munapanga chisankho
chomutumikila mulungu
kudzera mu mkuyimba tiyeni tipewe zinthu ngati izi
tisamalichitise manyazi dzina la mulungu.

(Visited 4 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram