1. They are good at appreciating a woman (i.e. Iwe mkazi mgwakukongola chomene)

2. TheY are faithful to their partners, very faithful

3. They are mature, act mature

4. Economical and Prudent

5. They are very good kissers. Samaluma when kissing

6. They are very good at Romance mwamva (dinda iyi imandifikapo pachoko)

7. They are clean

8. Amatha ma style (good at sex)

9. Sweet talk ndi more palibenso (ukamandisekelera mkazi ine ndimakumbuka malemu Kamuzu Banda)

10. Ambiri amakhala obeleka osati okugwa mumpapaya

11. Ophunzira

12. Amakwatira ali prepared basi osati kuthamangira

13. Samenya mkazi

14. sagoneka mkazi ndi njala

15. Amakonda kucheza ndiwokondedwa

(Visited 19 times, 1 visits today)
0

Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram