Iyi ndi kalata yomwe analemba DC wa boma la Mulanje yowopsyeza anthu ogwira ntchito ku District Council kuti akafuna kugwira ntchito za chitukuko aziyamba adziwitsa kaye Brown Mpinganjira yemwe ndi nduna yowona za chitukuko chamadzi yemwenso akufuna kuzayimila ngati phungu mdera lake ku Mulanje-ko.

DC anawopsyeza aliyense yemwe satsatila lamulori kuti zikazamuvuta zake zimenezo asazati sanamve.

mj dc

(Visited 14 times, 1 visits today)


Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram