Mphekesera ikumveka kuti Ma blacks (Black Missionaries) akuti dzulo akana kulandira ndalama zoti akamenye show ya ulere la mulungu Ku Blantyre pofuna kuti anthu ambiri asazapite Ku sonkhano wa UTM

Ma report akusonyeza  kuti Ma blacks ayankha kuti Ali ndi show ina ndipo sangawawuze zochita mu masiku ochepa kuti akaimbe pa mwambo wo tsegulira Kamuzu stadium.

Zikumveka kuti m’modzi mwa oyimba amene amafuna akathandizane ndi ma blacks anasankhidwa ndi katswiri Taygrin.

More to come…..

Subscribe to our Youtube Channel: