A Police ku Lilongwe akudziwitsa nonse kuti amanga officer wa security ku Parliament, Youngson Chilinde, kamba kosasantha makofu mtolankhani wa ku Nation Publications Limited, Thoko Banda.

Mtolankhani yu anamenyedwa makofu kumaso kufire ngati ngati waphoda magazi.

Youngson Chilinde akayankha mulandu wa Assault and battery

(Visited 2 times, 1 visits today)
Subscribe to our Youtube Channel :


Follow our Instagram