Zimene akuchita mayi Joyce Banda, palibe mtsogoleri olo m’modzi pa dziko lapansi pano anachitapo chawuta chililengereni dzikoli.

Mtsogoleri kumachita kupita kumudzi kwenikweni (deepest remote areas) ndikukakhalira mphatsa yeniyeniyi president zoona? Aaah abale, mtsogoleri sangapotse apa ayi winawu ndiye ufiti tsopano.

Mtsogoleri adzikonda anthu ake, kuchezera odwala ndi anthu olema, mtsogoleri azikadziwonera yekha umphawi wa anthu kumidzi monga achitira a Mayiwa osati zomakagula bonya kumsika ndikumanamiza anthu kuti ndinadyera mpunga koma atapatsa agalu.

MAYI JB, DZIKO NDI LANU ILI GWILANI NTCHITO!!!!

(Visited 22 times, 1 visits today)


Subscribe to our Youtube Channel :

Follow Us on Instagram